DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Nyimbo ya Solomo Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 6 Kalata Yoyamba Yopita kwa Timoteyo Machaputala 1 2 3 4 5 6 Mitu 1 Moni (1, 2) Chenjezo lokhudza aphunzitsi abodza (3-11) Paulo anasonyezedwa kukoma mtima kwakukulu (12-16) Mfumu yamuyaya (17) “Kumenya nkhondo yabwino” (18-20) 2 Kupempherera anthu osiyanasiyana (1-7) Mulungu mmodzi, mkhalapakati mmodzi (5) Dipo lokwanira ndendende (6) Malangizo kwa amuna ndi akazi (8-15) Kuvala mwaulemu (9, 10) 3 Zoyenera kuti munthu akhale woyangʼanira (1-7) Zoyenera kuti munthu akhale mtumiki wothandiza (8-13) Chinsinsi chopatulika cha kudzipereka kwa Mulungu (14-16) 4 Chenjezo lokhudza zomwe ziwanda zimaphunzitsa (1-5) Kukhala mtumiki wabwino wa Khristu (6-10) Kulimbitsa thupi ndiponso kudzipereka kwa Mulungu (8) Uzisamala ndi zimene umaphunzitsa (11-16) 5 Zoyenera kuchita ndi achikulire komanso achinyamata (1, 2) Kuthandiza akazi amasiye (3-16) Kusamalira banja (8) Kulemekeza akulu akhama (17-25) ‘Vinyo pangʼono, chifukwa cha vuto la mʼmimba’ (23) 6 Akapolo azilemekeza ambuye awo (1, 2) Aphunzitsi onyenga ndiponso kukonda ndalama (3-10) Malangizo kwa munthu wa Mulungu (11-16) Kulemera pa ntchito zabwino (17-19) Sunga zimene unalandira (20, 21) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena 1 Timoteyo— Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) 1 Timoteyo— Zimene Zili Mʼbukuli Chichewa 1 Timoteyo— Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt 1 Timothy pp. 2008-2009