Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Yobu Anachita Kuti Akhalebe Woyera

Zimene Yobu Anachita Kuti Akhalebe Woyera

Yobu anachita pangano ndi maso ake (Yob 31:1; w10 4/15 21 ¶8)

Yobu ankadziwa bwino mavuto amene angakhalepo chifukwa chochita zoipa (Yob 31:​2, 3; w08 9/1 11 ¶4)

Yobu ankakumbukira kuti Mulungu amaona zimene iye amachita (Yob 31:4; w10 11/15 5-6 ¶15-16)

Kukhala woyera kumatanthauza kulankhula komanso kuchita zinthu zoyenera. Koma si zokhazi, timafunikanso kukhala oyera mumtima.—Mt 5:28.