4-D
Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu M’Galileya (Gawo 2)
NTHAWI |
MALO |
CHOCHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
31 kapena 32 |
Kaperenao |
Yesu afotokoza mafanizo a Ufumu |
||||
Nyanja ya Galileya |
Aletsa mphepo yamkuntho ali m’ngalawa |
|||||
Dera la Gadara |
Atumiza ziwanda kuti zikalowe mu nkhumba |
|||||
Mwina ku Kaperenao |
Achiritsa mayi wina wa nthenda yotaya magazi; Aukitsa mwana wamkazi wa Yairo |
|||||
Kaperenao (?) |
Achiritsa wosaona ndi wosalankhula |
|||||
Nazareti |
Akanidwanso mu mzinda wakwawo |
|||||
Galileya |
Ulendo wachitatu woyendera Galileya; madera ambiri ayenderedwa atatumiza atumwi |
|||||
Tiberiyo |
Herode adula mutu wa Yohane M’batizi; Herode achita mantha atamva za Yesu |
|||||
32, Chikondwerero cha Pasika chitayandikira (Yoh. 6:4) |
Kaperenao (?); Kumpoto chakum’mawa kwa Nyanja ya Galileya |
Atumwi abwerako pa ulendo wokalalikira; Yesu adyetsa amuna 5,000 |
||||
Kumpoto chakum’mawa kwa Nyanja ya Galileya; Genesarete |
Anthu ayesa kulonga ufumu Yesu; ayenda panyanja; achiritsa anthu |
|||||
Kaperenao |
Afotokoza za “chakudya chopatsa moyo”; ophunzira ambiri akhumudwa ndi kusiya kum’tsatira |
|||||
32, Pambuyo pa Pasika |
Mwina ku Kaperenao |
Afotokoza za miyambo ya anthu |
||||
Foinike; Dekapole |
Achiritsa mwana wamkazi wa mayi wa ku Foinike; adyetsa anthu 4,000 |
|||||
Magadani |
Asaduki ndi Afarisi afuna chizindikiro |