4-F
Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki wa Yesu Wakumapeto Kum’mawa kwa Yorodano
NTHAWI |
MALO |
CHOCHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
32, pambuyo pa Chikondwerero Chopereka Kachisi kwa Mulungu |
Betaniya wa kutsidya kwa Yorodano |
Apita kumene Yohane ankabatizira; ambiri akhulupirira Yesu |
||||
Pereya |
Aphunzitsa m’mizinda ndi m’midzi, alowera ku Yerusalemu |
|||||
Awalimbikitsa kulowa pakhomo lopapatiza; adandaulira Yerusalemu |
||||||
Mwina ku Pereya |
Aphunzitsa kudzichepetsa; mafanizo: malo olemekezeka kwambiri ndi alendo omwe analephera kubwera ku phwando |
|||||
Kuwerengera mtengo wa kukhala wophunzira |
||||||
Mafanizo: nkhosa yotayika, ndalama yotaika, mwana wolowerera |
||||||
Mafanizo: Mtumiki woyang’anira nyumba wosalungama, munthu wolemera ndi Lazaro |
||||||
Aphunzitsa zokhudza kukhumudwitsana, kukhululukirana, ndi chikhulupiriro |
||||||
Betaniya |
Lazaro amwalira ndi kuukitsidwa |
|||||
Yerusalemu; Efuraimu |
Chiwembu chofuna kupha Yesu; achokako |
|||||
Samariya; Galileya |
Achiritsa akhate 10; aphunzitsa za Ufumu wa Mulungu |
|||||
Samariya kapena Galileya |
Mafanizo: mkazi wamasiye wolimbikira kupempha, Mfarisi ndi wokhometsa msonkho |
|||||
Pereya |
Aphunzitsa za ukwati ndi zokhudza kuthetsa ukwati |
|||||
Adalitsa ana aang’ono |
||||||
Funso la munthu wolemera; fanizo la antchito a m’munda wa mpesa ndi malipiro ofanana |
||||||
Mwina ku Pereya |
Kachitatu Yesu aneneratu za imfa yake |
|||||
Kupemphera malo Yakobo ndi Yohane mu Ufumu |
||||||
Yeriko |
Podutsa achiritsa amuna awiri osaona; achezera Zakeyu; fanizo la ndalama 10 za mina |