16-A
Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 1)
Nisani 8 (Sabata)
MADZULO (Masiku Achiyuda amayamba ndi kutha dzuwa litalowa)
-
Afika ku Betaniya masiku 6 Pasika asanachitike
M’MAWA
MADZULO
Nisani 9
MADZULO
-
Achita phwando panyumba ya Simoni wakhate
-
Mariya adzoza Yesu mafuta a nado
-
Ayuda afika kudzaona Yesu ndi Lazaro
M’MAWA
-
Khristu alowa mu Yerusalemu monga wopambana
-
Aphunzitsa pakachisi
MADZULO
Nisani 10
MADZULO
-
Akhala usiku wonse ku Betaniya
M’MAWA
-
Alawirira kupita ku Yerusalemu
-
Athamangitsa amalonda ogulitsa pa kachisi
-
Yehova alankhula kuchoka kumwamba
MADZULO
Nisani 11
MADZULO
M’MAWA
-
Akuphunzitsa mu kachisi, pogwiritsa ntchito mafanizo
-
Adzudzula mwamphamvu Afarisi
-
Kakhobidi ka mkazi wamasiye
-
Pa Phiri la Maolivi, aneneratu za kugwa kwa Yerusalemu ndi kunena za chimene chidzakhale chizindikiro cha kukhalapo kwake
MADZULO