Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2023-2024

Lowani mu Mpumulo wa Mulungu

Pulogalamu ya chigawo cha m’mawa komanso masana cha msonkhano wadera wokhala ndi woimira nthambi.

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mafunsowa adzayankhidwa pomwe msonkhanowu ukuchitika.