Musadzaphonye Kuwerenga Galamukani! Yotsatira
Kuyambira ndi Galamukani! ya January 2013, magazini ya Galamukani! izikhala ndi nkhani zosavuta kuwerenga, zithunzi zokongola komanso nkhani zina ngati: “Mfundo Zothandiza Mabanja,” “Kucheza ndi Anthu,” “Anthu Komanso Komwe Akuchokera” ndi “Zithunzi Zakale.” *
Nkhani zimene zidzatuluke mu Galamukani! ya January 2013
Mfundo Zothandiza Mabanja—“Zimene Mungachite Kuti Muzilankhulana Momasuka ndi Mwana Wanu Wachinyamata”
Kucheza ndi Anthu—“Wasayansi Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake”
Anthu Komanso Komwe Akuchokera—“Dziko la Cameroon”
^ ndime 2 Nkhani zina sizizidzatuluka mwezi uliwonse.