Mfundo Zina Zothandiza Makolo
Monga mwaonera, malangizo amene ali m’magaziniyi ndi ochokera m’Baibulo. M’Baibulo mumapezeka malangizo abwino kwambiri amene angathandize kuti banja likhale losangalala. Mfundo zake zimathandiza munthu kukhala woganiza bwino komanso kuti azisankha zinthu mwanzeru.—Miyambo 1:1-4.
BAIBULO LIMAYANKHANSO MAFUNSO OFUNIKA KWAMBIRI MONGA AKUTI:
Tikukulimbikitsani kuti mufufuze m’Baibulo mayankho a mafunso amenewa komanso ena. Onerani kavidiyo kakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? popanga sikani kachidindo aka kapena pitani pa www.ps8318.com.