Kodi Munayamba Mwadzifunsapo Kuti:
N’chifukwa chiyani padzikoli pali mavuto ambiri chonchi?
Kodi mungapeze kuti nzeru zokuthandizani kulimbana ndi mavuto?
Kodi Mulungu amasamala za inuyo panokha?—1 Petulo 5:6, 7.
Kodi mungadziwe bwanji zokhudza Mulungu ndi zimene amafuna?
Anthu mamiliyoni ambiri apeza mayankho othandiza a mafunso amenewa pophunzira Malemba Opatulika. Nanunso mukhoza kupeza mayankho a mafunsowa.
Ngati mukufuna kumva zambiri, pemphani amene amafalitsa magaziniyi kuti akupatseni kwaulere kabuku kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu kapenanso werengani kabukuka pa www.ps8318.com.