NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) April 2022
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira June 6–July 3, 2022.
NKHANI YOPHUNZIRA 15
Kodi Ndinu “Chitsanzo . . . M’kalankhulidwe”?
NKHANI YOPHUNZIRA 16
Muzisangalala ndi Zonse Zomwe Mukuchita Potumikira Yehova
NKHANI YOPHUNZIRA 17
Zimene Azimayi Angaphunzire kwa Yunike
NKHANI YOPHUNZIRA 18
Tingatani Kuti Tizikhala ndi Zolinga Zauzimu N’kumazikwaniritsa?
Mafunso Ochokera kwa Owerenga
Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani ya malumbiro?
Mafunso Ochokera kwa Owerenga
Ngati Mkhristu wathetsa banja osati pa zifukwa za m’Malemba n’kukwatirana ndi munthu wina, kodi mpingo umaona bwanji ukwati wakalewo komanso watsopanowo?