Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi Mulungu wachita zinthu zitatu ziti pofuna kuthetsa mavuto amene anthu akukumana nawo? ONANI TSAMBA 5-6.

Kodi mungachite zinthu ziti kuti mulimbikitse munthu amene waferedwa mwamuna kapena mkazi wake? ONANI TSAMBA 10-12.

N’chifukwa chiyani wotsatira wa Khristu ayenera kulalikira? ONANI TSAMBA 17.

Kodi mungachite chiyani kuti muthandize mwana wanu kuti akadzakula adzathe kudziimira payekha? ONANI TSAMBA 19.

Kodi n’chiyani chinachititsa kuti munthu wina amene poyamba sankafuna kumvera boma kapena kukhala mu mpingo uliwonse, asinthe n’kukhala mtumiki wa Mulungu? ONANI TSAMBA 28-29.