Tsamba 32
Tsamba 32
Kodi mungachite chiyani kuti mulimbikitse mnzanu amene akudwala kwambiri? ONANI TSAMBA 10-13.
Kodi Hana anali ndani, nanga chikhulupiriro chake chinamuthandiza bwanji kupirira zoipa zimene mkazi mnzake ankamuchitira? ONANI TSAMBA 14-18.
Kodi ndi chinthu chimodzi chiti chimene mungachite kuti mupindule ndi kuwerenga Baibulo? ONANI TSAMBA 19-21.
Kodi Mulungu ali ndi chiyambi? ONANI TSAMBA 28.
Kodi Mulungu amayang’ana chiyani mumtima mwathu? ONANI TSAMBA 29.