Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi n’chifukwa chiyani tifunika kukhala ndi mtima woyamikira? ONANI TSAMBA 6.

Kodi munganene chiyani potonthoza mnzanu kapena wachibale amene waferedwa? ONANI TSAMBA 9-11.

Kodi angelo amachita chidwi ndi anthufe? ONANI TSAMBA 16.

N’chifukwa chiyani Baibulo la Dziko Latsopano limalemekeza Mulungu? ONANI TSAMBA 26.

Kodi Yesu amafuna kuti otsatira ake akhale m’gulu linalake la chipembedzo? ONANI TSAMBA 31.