NSANJA YA OLONDA July 2011 Kodi Moyo Uli Ndi Phindu Lililonse? Kodi N’chifukwa Chiyani Moyo Umaoneka Ngati Wopanda Phindu? N’zotheka Kukhala Wosangalala Panopa Komanso Kwamuyaya YANDIKIRANI MULUNGU Kodi Yehova Amasangalala Kapena Kukhumudwa Ndi Zochita Zathu? Baibulo Limasintha Anthu Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? Analimbikitsidwa Ndi Mulungu Wake Kodi Mulungu Amaona Kuti Mtundu Wina Wa Anthu Ndi Wofunika Kuposa Mitundu Ina? Kodi Ndani Anakhazikitsa Malamulo a Zinthu Zakuthambo? Kodi Mukudziwa? Zimene Mungachite Mukakumana Ndi Mayesero