Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo

Mumavidiyo amenewa, onani zimene mungaphunzire kwa amuna ndi akazi okhulupirika otchulidwa m’Baibulo.

Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Abulahamu, Mbali Yoyamba

Muvidiyoyi, onani mmene Abulahamu anasonyezera kuti sankakayikira ngakhale pang’ono kuti Yehova amakwaniritsa zonse zomwe walonjeza.

Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Abulahamu, Mbali Yachiwiri

Muvidiyoyi, onani mmene Yehova anadalitsira Abulahamu komanso mmene anadalitsira anthu onse kudzera mwa iye.

Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Rabeka

Kodi chikhulupiriro cha Rabeka chimuthandiza kuti achoke kwawo n’kupita kudziko limene sakulidziwa?

Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Miriamu

Tonsefe timalakwitsa zinthu nthawi zina ndipo ndi mmenenso zinalili ndi Miriamu. Onani mmene kukhulupirira Yehova kunamuthandizira kuti alandire chilango.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

KUKHULUPIRIRA MULUNGU

Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Amuna ndi Akazi Otchulidwa M’Baibulo

Muzitengera zitsanzo za amuna ndi akazi okhulupirika otchulidwa m’Baibulo kuti muyandikire Mulungu.