Mfundo Zachidule—South Korea
- 51,408,000—Chiwerengero cha anthu
- 106,161—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 1,252—Mipingo
- Pa anthu 485 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
Akhristu a ku South Korea Anakana Kulowa Usilikali—Nkhani Yosonyeza Chikhulupiriro ndi Kulimba Mtima Kwawo
Kuyambira mu 1953, abale achinyamata a ku Korea akhala akumangidwa chifukwa chokana kulowa usilikali potsatira zomwe amakhulupirira. Koma mu February 2019, zinthu zinasintha. Kodi zinthu zosaiwalikazi zinatheka bwanji?