Mfundo Zachidule—Namibia
- 2,680,000—Chiwerengero cha anthu
- 2,711—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 47—Mipingo
- Pa anthu 1,030 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
M’chigawo cha Kunene, ku Namibia—Akulalikira anthu a mtundu wa Chihimba pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha, m’chinenero cha Chiherero