Patha Zaka 50 Tili ku Wallkill YAMBANI Patha Zaka 50 Tili ku Wallkill Dziwani mbiri ya famu imene yakhala ikutulutsa zokolola zapadera kwa zaka zambiri. Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi MOYO WA PA BETELI Tikukuitanani Kuti Mudzaone Maofesi Athu ku United States Mudzaonanso Likulu la Padziko Lonse la Mboni za Yehova lomwe lili ku United States. MOYO WA PA BETELI Mafamu a Watchtower Akhala Akuthandiza Kwambiri kwa Zaka 50 Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene famuyi yasinthira kwa zaka zambiri kuti ithandize pa ntchito ya padziko lonse yophunzitsa anthu Baibulo imene a Mboni za Yehova amachita. NTCHITO ZOMANGAMANGA Ntchito Yomanga Ikuyenda Bwino Kwambiri ku Wallkill ndi ku Warwick Ntchito yaikulu yomanga nyumba ndi maofesi atsopano a Mboni za Yehova ku United States ikuyenda bwino kwambiri. Ntchitoyi ikuchitika m’malo awiri ndipo anthu ongodzipereka, ochokera m’dziko lomweli, ndi amene akugwira ntchitoyi. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Patha Zaka 50 Tili ku Wallkill MOYO WA PA BETELI Patha Zaka 50 Tili ku Wallkill Chichewa Patha Zaka 50 Tili ku Wallkill https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502014182/univ/art/502014182_univ_sqr_xl.jpg