Wosaona Ndiponso Wosamva
James Ryan, yemwe ndi wa Mboni za Yehova, anabadwa ndi vuto losamva ndipo kenako anakhalanso ndi vuto losaona. Onerani vidiyoyi kuti mudziwe chifukwa chimene amaonera kuti anthu a m’banja lake ndi a mumpingo, * akumuthandiza kuti asamadzione ngati wopanda pake.
^ ndime 2 Pa anthu onse a m’banja la James, wa Mboni ndi yekha.