Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

MAY 23, 2018
ITALY

Kufunsa a Pulofesa Antonio D. Pinna, M.D.

Kufunsa a Pulofesa Antonio D. Pinna, M.D.

A Pinna ndi katswiri wopanga opaleshoni ndi kuika ziwalo m’thupi pa Yunivesite ya Bologna, mkulu wa madokotala opanga maopaleshoni osiyanasiyana komanso woika ziwalo za m’thupi pa chipatala cha Policlinico S. Orsola-Malpighi ku Bologna. Iwowa amapanganso opaleshoni ya chiwindi ndi ndulu komanso amaika ziwalo za m’thupi pa bungwe lina (Digestive Disease Institute) pa chipatala cha Cleveland ku Abu Dhabi.