Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tingakhale na Mtima Wosagaŵikana Ngakhale Ndife Opanda Ungwilo

Tingakhale na Mtima Wosagaŵikana Ngakhale Ndife Opanda Ungwilo

Yobu anaimba Mulungu mlandu (Yobu 27:​1, 2)

Yobu anali na mtima wosagaŵikana ngakhale kuti analakwitsapo zinthu zina (Yobu 27:5; it-1 1210 ¶4)

Kukhala na mtima wosagaŵikana kumafuna kumukonda na mtima wonse Yehova, osati kukhala angwilo (Mat. 22:37; w19.02 3 ¶3-5)

ZOYENELA KUZISINKHASINKHA: Kodi kudziŵa kuti Yehova satiyembekezela kucita zinthu mwangwilo kumatithandiza bwanji kusalefuka?