Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’

‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’

Elifazi anakamba kuti Mulungu amationa ngati opanda pake (Yobu 22:​1, 2; w05 9/15 27 ¶1-3)

Iye anakambanso kuti Mulungu sasamala zakuti ndife olungama kapena ayi (Yobu 22:3; w95 2/15 27 ¶6)

Mwa zocita zathu, Yehova akhoza kumuyankha Satana, amene amamutonza (Miy. 27:11; w03 4/15 14-15 ¶10-12)

ZOYENELA KUZISINKHASINKHA: Kodi mumamva bwanji kudziŵa kuti ndinu wofunika kwa Wamphamvuzonse?