Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Loŵani mu Mpumulo wa Mulungu!

Loŵani mu Mpumulo wa Mulungu!

AHEBERI 4:11

M’maŵa

  • 08:40 Nyimbo Zamalimba

  • 08:50 Nyimbo Na. 87 na Pemphelo

  • 09:00 Loŵani mu Mpumulo wa Mulungu —Motani?

  • 09:15 Kodi “Mawu a Mulungu ndi Amoyo”—M’njila Yotani?

  • 09:30 Pitilizani Kudalila Yehova Kuti Akutsogoleleni

  • 09:55 Nyimbo Na. 89 na Zilengezo

  • 10:05 Yehova Amadalitsa anthu Omvela

  • 10:35 Kudzipatulila na Ubatizo

  • 11:05 Nyimbo Na. 32

Masana

  • 12:20 Nyimbo Zamalimba

  • 12:30 Nyimbo Na. 49

  • 12:35 Zocitika

  • 12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 13:15 Nkhani Yosiyilana: Amakondweletsa Mtima wa Yehova!

    • • Acinyamata

    • • Alongo

    • • Okalamba

  • 14:00 Nyimbo Na. 38 na Zilengezo

  • 14:10 Pezani Cimwemwe mu Utumiki Wanu kwa Yehova

  • 14:55 Nyimbo Na. 118 na Pemphelo