Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa 2023 wa Mutu Wakuti “Khalani Oleza Mtima”

Tsiku Loyamba

Pulogilamu ya tsiku loyamba yazikidwa pa 1 Akorinto 13:4—“Cikondi n’coleza mtima.”

Tsiku Laciŵili

Pulogilamu ya tsiku laciŵili yazikidwa pa 1 Atesalonika 5:14—“Khalani oleza mtima kwa onse.”

Tsiku Lacitatu

Pulogilamu ya tsiku lacitatu yazikidwa pa Yesaya 30:18—“Yehova azidzayembekezela kuti akukomeleni mtima.”

Mawu kwa Osonkhana

Mawu othandiza kwa opezeka pa msonkhano wacigawo.

Mungakondenso Izi

ZOKHUDZA IFE MBONI

Kapezekemponi pa Msonkhano wa Cigawo wa 2024 wakuti​—Lengezani Uthenga Wabwino!

Tikuitanilani kuti mukapezeke ku msonkhano wa cigawo wa Mboni za Yehova wa masiku atatu.

MISONKHANO IKULUIKULU

Tikuitanilani ku Msonkhano Wacigawo wa Mboni za Yehova wa 2023 wa Mutu Wakuti “Khalani Oleza Mtima”!

Conde mukabwele ku msonkhano wacigawo caka cino wa masiku atatu wa Mboni za Yehova.

MISONKHANO IKULUIKULU

Kadyonkho ka Seŵelo Lakuti ‘Lola Yehova Akutsogolele Panjila Yako’

Phunzilani mmene zovuta zimene tingakumane nazo zingalimbikitsile cidalilo cathu mwa Yehova.