4-H
Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko—Utumiki Womaliza wa Yesu m’Yerusalemu (Mbali 2)
NTHAWI |
MALO |
COCITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
Nisani 14 |
Yerusalemu |
Yesu azindikila Yudasi kukhala wom’peleka ndipo amuuza kuti acoke |
22:21-23 |
13:21-30 |
||
Akhazikitsa M’gonelo wa Cakudya ca Ambuye (1 Akor. 11:23-25) |
22:19, 20, 24-30 |
|||||
Anenelatu za kukanidwa ndi Petulo ndi za kuthawa kwa atumwi |
22:31-38 |
13:31-38 |
||||
Alonjeza mthandizi; fanizo la mpesa weniweni; apeleka lamulo lokondana; pemphelo lomaliza ndi atumwi |
14:1–17:26 |
|||||
Getsemane |
Nkhawa yaikulu m’munda; Kupelekedwa kwa Yesu ndi kumangidwa |
22:39-53 |
18:1-12 |
|||
Yerusalemu |
Afunsidwa ndi Anasi; ayesedwa ndi Kayafa, Sanihedrini; Petulo am’kana |
22:54-71 |
18:13-27 |
|||
Yudasi wom’peleka adzimangilila yekha (Mac. 1:18, 19) |
||||||
Aonekela kwa Pilato, ndiyeno kwa Herode, ndipo am’bwezanso kwa Pilato |
23:1-12 |
18:28-38 |
||||
Pilato ayesa kum’masula koma Ayuda apempha kuti amasule Baraba; amupha pamtengo wonzunzilapo |
23:13-25 |
18:39–19:16 |
||||
(c. 3:00 masana., Cisanu) |
Gologota |
Akufa pamtengo wonzunzilapo |
23:26-49 |
19:16-30 |
||
Yerusalemu |
Acotsa mtembo pamtengo ndi kuika m’manda |
23:50-56 |
19:31-42 |
|||
Nisani 15 |
Yerusalemu |
Ansembe ndi Afalisi aika asilikali olondela manda ndi kutsekapo |
||||
Nisani 16 |
Yerusalemu ndi madela apafupi; Emau |
Yesu aukitsidwa; aonekela nthawi zisanu kwa ophunzila ake |
24:1-49 |
20:1-25 |
||
Pambuyo pa Nisani 16 |
Yerusalemu; Galileya |
Aonekelanso nthawi zambili kwa ophunzila (1 Akor. 15:5-7; Mac. 1:3-8); apeleka malangizo; awatuma kuti akapenge ophunzila |
20:26–21:25 |
|||
Iyara 25 |
Phili la Maolivi, pafupi ndi Betaniya |
Pambuyo pa masiku 40 ataukitsidwa Yesu akwela kumwamba (Mac. 1:9-12) |
24:50-53 |