4-G
Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko—Utumiki Womaliza wa Yesu m’Yerusalemu (Mbali 1)
NTHAWI |
MALO |
COCITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
33, Nisani 8 |
Betaniya |
Yesu afika masiku 6 Pasika asanayambe |
11:55–12:1 |
|||
Nisani 9 |
Betaniya |
Mariya athila mafuta m’mutu wa Yesu ndi kumapazi ake |
12:2-11 |
|||
Betaniya-Betefage- Yerusalemu |
Aloŵa mu Yerusalemu mwacisangalalo, atakwela bulu |
19:29-44 |
12:12-19 |
|||
Nisani 10 |
Betaniya-Yerusalemu |
Atembelela mtengo wa nkhuyu; ayeletsanso kacisi |
19:45, 46 |
|||
Yerusalem Mkulu wansembe ndi alembi akonza ciwembu cofuna kupha Yesu |
19:47, 48 |
|||||
Yehova alankhula; Yesu anenelatu za imfa yake; kusakhulupilila kwa Ayuda kukwanilitsa ulosi wa Yesaya |
12:20-50 |
|||||
Nisani 11 |
Betaniya-Yerusalemu |
Phunzilo la mtengo wa mkuyu wofota |
||||
Yerusalemu, kacisi |
Atsutsa ulamulilo wake; mafanizo a ana aŵili |
20:1-8 |
||||
Mafanizo: alimi akupha, phwando la cikwati |
20:9-19 |
|||||
Ayankha mafunso onena za Mulungu ndi Kaisara, ciukililo, lamulo lalikulu |
20:20-40 |
|||||
Afunsa khamu la anthu ngati Kristu ndi mwana wa Davide |
20:41-44 |
|||||
Tsoka alembi ndi Afalisi |
20:45-47 |
|||||
Aona copeleka ca mkazi wamasiye |
21:1-4 |
|||||
Phili la Maolivi |
Apeleka cizindikilo ca kubwela kwake kwa mtsogolo |
21:5-38 |
||||
Mafanizo: Anamwali 10, matalente, nkhosa ndi mbuzi |
||||||
Nisani 12 |
Yerusalemu |
Atsogoleli aciyuda akonza ciwembu cofuna kumupha |
22:1, 2 |
|||
Yudasi alinganiza zom’peleka |
22:3-6 |
|||||
Nisani 13 (Cinai masana) |
Mu Yerusalemu ndi capafupi |
Akonzekela Pasika womaliza |
22:7-13 |
|||
Nisani 14 |
Yerusalemu |
Akudya mgonelo ndi atumwi ake |
22:14-18 |
|||
Asambika mapazi a ophunzila ake |
13:1-20 |