Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale Ndi Moyo Wamuyaya
Mlengi wathu amafuna kutitsogolela, kutiteteza, na kutidalitsa.
Mau Oyamba
Cifukwa cakuti amakonda anthu, Mulungu amatiphunzitsa mmene tingakhalile na umoyo wabwino.
Kodi Tingamumvetsele Bwanji Mulungu?
Tifunika kudziŵa cimene tiyenela kucita ndi amene angatithandize kucita zimenezo.
Kodi Mulungu Woona Ndani?
Tingathe kudziŵa dzina lake na makhalidwe ake.
Kodi Umoyo Unali Bwanji m’Paladaiso?
Buku loyamba m’Baibo limafotokoza mmene umoyo unalili m’Paladaiso.
Anamvetsela kwa Satana—Nanga Cinacitika n’Ciani?
Mavuto anayamba.
Cigumula ca Nowa—Ndani Anamvetsela? Ndani Sanamvetsele?
Ni kusiyana kotani pakati pa anthu kumene kunaonekela bwino?
Kodi Cigumula ca Nowa Cimatiphunzitsa Ciani?
Si nkhani yopeka, inacitikadi.
Kodi Yesu Anali Ndani?
N’cifukwa ciani kuphunzila za Yesu n’kofunika?
Kodi Tingapindule Bwanji Ndi Imfa ya Yesu?
Inacititsa kuti tikhale na mwayi wokalandila madalitso osaneneka.
Kodi Paladaiso Idzabwela Liti?
Baibo inakambilatu zimene zidzacitika ngati paladaiso yatsala pang’ono kubwela.
Kodi Anthu Amene Amamvetsela kwa Mulungu Adzapeza Madalitso Abwanji?
Madalitso am’tsogolo amene simufunika kuwaphonya.
Kodi Yehova Amamvetsela kwa Ife?
N’zinthu zabwanji zimene mungam’pemphe Mulungu?
Mungacite Ciani Kuti Banja Likhale Lokondweletsa?
Mlengi amapeleka malangizo abwino ngako cifukwa ndiye anayambitsa banja.
Kodi Tiyenela Kucita Ciani Kuti Tikondweletse Mulungu?
Pali zinthu zina zimene amazonda, na zina zimene amakonda.
Kodi Mungaonetse Bwanji Kuti Ndinu Okhulupilika kwa Yehova?
Mufunika kuonetsa mwa zosankha zanu kuti mumafuna kukhala okhulupilika.