Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

GALAMUKA! Na. 2 2019 | Zinthu 6 Zimene Ana Afunika Kuphunzila

Zinthu 6 Zimene Ana Afunika Kuphunzila

Kodi mwana wanu akadzakula, mungakonde kuti akakhale munthu wotani?

  • Wodziletsa

  • Wodzicepetsa

  • Wolimbikila

  • Waudindo

  • Wokhwima m’Maganizo

  • Woona mtima

Ana sangakhale na makhalidwe amenewa paokha. Afunikila thandizo lanu.

Magazini ino idzafotokoza zinthu 6 zimene mufunika kuphunzitsa ana anu kuti akule bwino.

 

Mapindu a Kudziletsa

N’cifukwa ciani kudziletsa n’kofunika kwambili? Nanga tingacite ciani kuti tikhale na khalidwe limeneli?

Mmene Angakhalile Odzicepetsa

Kuphunzitsa ana anu kukhala odzicepetsa kudzaŵathandiza pali pano, komanso kutsogolo akadzakula.

Mmene Angakhalile Olimbikila

Ana amene amaphunzila kukhala olimbikila, amapilila bwino mavuto a mu umoyo.

Mmene Angakhalile Audindo

Kodi munthu afunika kuphunzila kukhala waudindo panthawi iti, akali wamng’ono kapena akakula?

Citsogozo ca Anthu Acikulile N’cofunikila

Ana amafunikila citsogozo codalilika mu umoyo. Koma kodi angacipeze kuti?

Kufunika kwa Makhalidwe Abwino

Mukaphunzitsa ana anu makhalidwe abwino, ndiye kuti mwaŵapangila maziko olimba a tsogolo lawo.

Malangizo Owonjezela kwa Makolo

Makolo nawonso afunika citsogozo codalilika kuti akhale na umoyo wopindulitsa. Kuti mudziŵe zambili, yendani pa jw.org.