NSANJA YA MLONDA Na. 1 2020 | Kufuna-funa Coonadi
Baibo imapeleka mayankho a zoona pa mafunso ena ofunika kwambili pa umoyo.
Kufuna-funa Coonadi
M’dzikoli, anthu sakhulupililana ndipo zambili zimene anthu amauzidwa sizikhala zoona. Koma pali njila imene mungaseŵenzetse kuti mupeze mayankho a zoona pa mafunso ofunika kwambili mu umoyo.
Baibo ni Gwelo Lodalilika la Coonadi
Mungakhale na cidalilo conse cakuti zimene Baibo imakamba mungazikhulupilile.
Coonadi Ponena za Mulungu na Khristu
Kodi pali kusiyana kotani pakati pa Yehova Mulungu na Yesu Khristu?
Coonadi Ponena za Ufumu wa Mulungu
Malemba amachula Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Komanso amafotokoza zoona za kumene kuli ufumuwo, colinga cake, olamulila ake, ndiponso nzika zake.
Coonadi Ponena za Kutsogolo
Limbitsani ciyembekezo canu pa zimene Mulungu amakamba ponena za tsogolo la dziko, komanso tsogolo la anthu amene adzakhala m’dzikolo.
Mmene Coonadi Cingakuthandizileni
Kudziŵa coonadi copezeka m’Mawu a Mulungu kungakubweletseleni mapindu ambili.