Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mmene Coonadi Cingakuthandizileni

Mmene Coonadi Cingakuthandizileni

Mulungu amene sanganame, akukupatsani ciyembekezo ca “moyo wosatha.”​—Yohane 3:16.

KODI MUYENELA KUCITA CIANI?

  •  Phunzilani Mawu a Mulungu, amene ni coonadi.—Yohane 17:3, 17.

  •  Sankhani kumvela Mulungu. —Deuteronomo 30:19, 20.

  •  Muziseŵenzetsa malangizo othandiza a Mulungu mu umoyo wanu.—Yakobo 1:25.

Mboni za Yehova pa dziko lonse lapansi zapindula cifukwa cophunzila coonadi ca m’Baibo. Iwo ni okonzeka kukuuzankoni zimene amaphunzila.

Kuti mudziŵe zambili zokhudza colinga ca Mulungu kwa anthu, onani nkhani 3 m’buku lakuti Zimene Baibulo Ingatiphunzitse, yolembewa na Mboni za Yehova. Ipezekanso pa webusaiti ya www.ps8318.com.