NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA September 2015

Magaziniyi ili ndi nkhani zophunzila kuyambila mlungu wa October 26 mpaka November 29, 2015.

Kodi Munafikapo pa Ucikulile Umene Kristu Anafikapo?

Ngakhale kuti tatumikila Yehova kwa nthawi yaitali, tifunika kupitiliza kukula kuuzimu.

Kodi Cikumbumtima Canu N’codalilika?

Onani mmene cingakuthandizileni kupanga zosankha za nzelu pa nkhani ya cithandizo ca mankhwala, zosangulutsa, ndi pa nchito yolalikila.

“Limbani m’Cikhulupililo”

Kodi citsanzo ca Petulo pamene anayenda pamadzi citiphunzitsa ciani pankhani ya cikhulupililo?

Kodi Yehova Waonetsa Bwanji Kuti Amatikonda?

Kodi zimakuvutani kukhulupilila kapena kuvomeleza kuti Yehova amakukondani?

Tingaonetse Bwanji Kuti Timakonda Yehova?

Tifunika kucita cinthu cina osati kungomvela mumtima.