NSANJA YA MLONDA July 2015 | Kodi Dzikoli Lili Pafupi Kutha?

Mukamva zakuti “Mapeto ali pafupi” mumaganiza za ciani? Kodi zimakucititsani mantha?

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi “Mapeto A Dziko” N’ciani?

Kodi mumadziŵa kuti zimene Baibulo limanena pa za “mapeto” ndi nkhani yabwino?

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Mapeto a Dzikoli Ali Pafupi?

Onani zizindikilo zinai zokhudza mapeto zofotokozedwa m’Baibulo zimene zikupeleka yankho

NKHANI YA PACIKUTO

Ambili Adzapulumuka—Nanga Bwanji Inuyo?

Adzapulumuka motani? Mwa kusunga zinthu kapena kudzikonzekeletsa mwakuthupi?

Zimene Mungacite Kuti Muzisangalala Paukalamba Wanu

Mfundo 6 za m’Baibulo zingakuthandizeni kusangalala pa ukalamba wanu.

BAIBO IMASINTHA ANTHU

Ndinaphunzila Kuti Yehova ndi Wacifundo ndi Wokhululukila

Kucita zacinyengo kunali ngati cakudya kwa Normand Pelletier. Koma ataŵelenga vesi limodzi m’Baibulo anagwetsa misozi.

Kodi Wokana Kristu Ndani?

Kodi adzabwela mtsogolo kapena akhala alipo kwa nthawi yonseyi?

Kuyankha Mafunso A m’Baibulo

Kodi mungaphunzitse bwanji ana anu kuti adzathe kudziimila paokha?