Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Thailand

78/12 Soi 31 Serithai Road

Bungkum

BANGKOK 10 240

THAILAND

+66 2-375-2200

+66 2-732-4971

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi

Zimene Timacita

Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Cithai, Cilaotiya, ndi Cilahu. Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova m’dzikoli ndi ku Laos.

Tengani kapepala koonetsa malo.